ALFRED GANGATA: WOTSUTSIDWA PA MSCE CERTIFICATE ATULUTSIDWA PA BELO!
Alfred Gangata Wapatsidwa Pabelo Ku Lilongwe
Panali chisangalalo panja pa bwalo la Chief Resident Magistrate ku Lilongwe lero, pomwe oweruza milandu Austin Banda anapereka pabelo kwa mtsogoleri wa chipani cha DPP m'chigawo chapakati, Alfred Gangata.
Gangata adamangidwa Lolemba chifukwa cha mlandu womuganizira kuti munthuwina adamulembera mayeso a Malawi School Certificate of Education (MSCE) mu chaka cha 2018.
Atatulutsidwa pabelo, anzake ndi otsatira ake anasonkhana panja pa bwaloli kukondwerera chisankho cha khothi.
Видео ALFRED GANGATA: WOTSUTSIDWA PA MSCE CERTIFICATE ATULUTSIDWA PA BELO! канала UMATHA DAILY

Комментарии отсутствуют
Информация о видео
21 марта 2025 г. 0:49:28
00:01:02
Другие видео канала